Haggai 2:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mulibe chakudya chambiri m'nkhokwe. Mpesa, mkuyu, makangaza ndiponso mtengo wa olivi zikali zosabereka. Koma kuyambira lero ndidzakudalitsani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mbeu ikali m'nkhokwe? Ngakhale mpesa, ndi mkuyu, ndi khangaza ndi azitona sizinabala; kuyambira lero lino ndidzakudalitsani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi mʼnkhokwe mwatsala mbewu? Mpaka lero, mpesa ndi mtengo wa mkuyu, makangadza ndi mtengo wa olivi sizinabereke zipatso. “ ‘Kuyambira lero mpaka mʼtsogolo ndidzakudalitsani.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mbeu ikali m'nkhokwe? Ngakhale mpesa, ndi mkuyu, ndi khangaza ndi mzitona sizinabala; kuyambira lero lino ndidzakudalitsani.