Haggai 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Umuuze Zerubabele bwanamkubwa wa ku Yuda, kuti ndidzagwedeza mlengalenga ndi dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi Zerubabele chiwanga cha Yuda, kuti, Ndidzagwedeza miyamba ndi dziko lapansi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uza Zerubabeli, bwanamkubwa wa Yuda, kuti ndidzagwedeza thambo ndi dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi Zerubabele ciwanga ca Yuda, kuti, Ndidzagwedeza miyamba ndi dziko lapansi;