Haggai 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musachite mantha, popeza kuti mzimu wanga uli pakati panu, monga momwe ndidalonjezera pamene munkatuluka ku Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
monga momwe ndinapangana nanu muja munatuluka m'Ejipito, ndi Mzimu wanga unakhala pakati pa inu; musamaopa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Izi ndi zimene ndinapangana nanu pamene munkatuluka ku Igupto. Ndipo Mzimu wanga uli pakati panu. Musachite mantha.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
monga momwe ndinapangana nanu muja munaturuka m'Aigupto, ndi Mzimu wanga unakhala pakati pa inu; musamaopa inu.