Haggai 2:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Siliva yense ndi wanga, golide yense ndi wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Siliva ndi wanga, ya golide ndi wanga, ati Yehova wa makamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Siliva yense ndi wanga, golide yense ndi wanganso,’ akutero Yehova Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Siliva ndi wanga, golidi ndi wanga, ati Yehova wa makamu.