Hebrews 1:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatinso, “Inu Ambuye, ndinu amene mudalenga dziko lapansi pachiyambi pomwe, zakumwambaku ndi ntchito ya manja anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo, Inu, Ambuye, pachiyambipo munaika maziko ake a dziko, ndipo miyamba ili ntchito ya manja anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu akutinso, “Ambuye, pachiyambi Inu munayika maziko a dziko lapansi; ndipo zakumwambako ndi ntchito za manja anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo, Inu, Ambuye, paciyambipo munaika maziko ace a dziko, Ndipo miyamba iri nchito ya manja anu;