Hebrews 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zidzatha, koma Inu ndinu achikhalire. Zonsezi zidzafwifwa ngati chovala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iyo idzataika; komatu mukhalitsa; ndipo iyo yonse idzasuka monga malaya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zimenezi zidzatha, koma Inu ndinu wachikhalire. Izo zidzatha ngati zovala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iyo idzatayika; komatu mukhalitsa; Ndipo iyo yonse idzasuka mongamaraya;