Hebrews 1:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzazipindapinda ngati mwinjiro, ndipo zidzasinthika ngati chovala, koma Inu ndinu osasinthika, zaka zanu sizidzatha konse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi monga chofunda mudzaipinda monga malaya, ndipo idzasanduka; koma Inu ndinu yemweyo, ndipo zaka zanu sizidzatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzazipindapinda ngati chofunda; ndipo zidzasinthidwa ngati chovala. Koma Inu simudzasintha, ndipo zaka zanu sizidzatha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi monga copfunda mudzaipinda Monga maraya, ndipo idzasanduka; Koma Inu ndinu yemweyo, Ndipo zaka zanu sizidzatha.