Hebrews 1:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkale lonse Mulungu sadauzepo mngelo aliyense kuti, “Khala ku dzanja langa lamanja mpaka ndisandutse adani ako kuti akhale ngati chopondapo mapazi ako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma za mngelo uti anati nthawi iliyonse, Khala pa dzanja lamanja langa, Kufikira ndikaika adani ako mpando wa kumapazi ako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndi kwa Mngelo uti kumene Mulungu ananenapo kuti, “Khala kudzanja langa lamanja mpaka nditapanga adani ako kukhale chopondapo mapazi ako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma za mngelo uti anati nthawi iri yonse, Khala pa dzanja lamanja langa, Kufikira ndikaika adani ako mpando wa ku mapazi ako?