Hebrews 1:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo za angelo Mulungu adati, “Mulungu amasandutsa angelo ake mphepo, atumiki ake amaŵasandutsa malaŵi a moto.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo za angelo anenadi, Amene ayesa angelo ake mizimu, ndi omtumikira Iye akhale malawi amoto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ponena za angelo akuti, “Mulungu amasandutsa angelo ake mphepo, amasandutsa atumiki ake malawi amoto.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo za angelo anenadi, Amene ayesa angelo ace mizimu, Ndi omtumikira iye akhale lawi lamoto;