Hebrews 10:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Mulungu wakhululukira zonsezi, sipafunikanso nsembe yoperekera machimo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pomwe pali chikhululukiro cha machimo palibenso chopereka cha kwa uchimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo pamene machimo akhululukidwa, sipafunikanso nsembe yoperekedwa chifukwa cha machimowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pomwe pali cikhululukiro ca macimo palibenso copereka ca kwaucimo.