Hebrews 10:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adatitsekulira njira yatsopano ndi yamoyo yobzola chochinga, chimene chili thupi lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pa njira yatsopano ndi yamoyo, imene adatikonzera, mwa chotchinga, ndicho thupi lake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatitsekulira njira yatsopano ndi yamoyo kudutsa chinsalu chotchinga, chimene ndi thupi lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pa njira yatsopano ndi yamoyo, imene adatikonzera, mwa cocinga, ndico thupi lace;