Hebrews 10:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tizikumbukirana kuti tilimbikitsane kukondana ndi kuchita ntchito zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo tiganizirane wina ndi mnzake kuti tifulumizane ku chikondano ndi ntchito zabwino,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tiziganizira mmene tingalimbikitsirane wina ndi mnzake pokondana ndi kuchita ntchito zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo tiganizirane wina ndi mnzace kuti tifulumizane ku cikondano ndi nchito zabwino,