Hebrews 10:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma monga zilirimu, nsembezo zimakumbutsa anthu za machimo ao chaka ndi chaka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu mu izizo muli chikumbukiro cha machimo chaka ndi chaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma nsembezo zimawakumbutsa anthuwo machimo awo chaka ndi chaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu mu izizo muli cikumbukiro ca macimo caka ndi caka.