Hebrews 10:37 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Malembo akuti, “Pangotsala kanthaŵi pang'ono chabe kuti Iye amene alikudza, afike. Sachedwa ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti katsala kanthawi kakang'onong'ono, ndipo wakudzayo adzafika, wosachedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti nʼkanthawi kochepa chabe, Iye amene akubwera adzabwera ndipo sadzachedwa ayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
9 Pakuti katsala kanthawi kakang'onong'ono, Ndipowakudzayoadzafika, wesacedwa.