Hebrews 10:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wolungama wanga adzakhala ndi moyo pakukhulupirira. Koma akamachita mantha nkubwerera m'mbuyo, Ine sindikondwera naye.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wolungama wangayo adzakhala ndi moyo wochokera m'chikhulupiriro: Ndipo ngati abwerera, moyo wanga ulibe kukondwera mwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma wolungama wangayo adzakhala ndi moyo mwachikhulupiriro. Ndipo ngati iye abwerera mʼmbuyo chifukwa cha mantha, Ine sindidzakondwera naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
10 Koma wolungama wangayo adzakhala ndi moyo wocokera m'cikhulupiriro: Ndipo ngati abwerera, moyo wanga ulibe kukondwera mwaiye.