Hebrews 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Magazi a ng'ombe zamphongo ndi a atonde sangathe konse kuchotsa machimo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti sikutheka kuti mwazi wa ng'ombe zamphongo, ndi mbuzi ukachotsera machimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa nʼkosatheka kuti magazi angʼombe yayimuna ndi mbuzi yayimuna achotse machimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti sikutheka kuti mwazi wa ng'ombe zamphongo, ndimbuzi ukacotsera macimo.