Hebrews 11:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja anthu olankhula motere, amaonekeratu kuti akufunafuna malo ao enieni okhazikikamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iwo akunena zotere aonetserapo kuti alikufuna dziko likhale lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amene amanena zinthu zotere amaonekeratu kuti akufuna dziko lawo lenileni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti wo akunena zotere aonetserapo kuti alikufuna dziko likhale lao.