Hebrews 11:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akadakhala kuti ankaganizirako za kudziko kumene adaachokera, bwenzi atapeza danga lakuti abwerere kwakaleko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipotu akadakumbukira lijalo adatulukamo akadaona njira yakubwera nayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akanakhala kuti akuganizira za dziko limene analisiya akanapeza mpata obwerera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipotu akadakumbukila lijalo adaturukamo akadaona njira yakubwera nayo.