Hebrews 11:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Za mwana ameneyu Mulungu anali atanena kuti, “Mwa Isaki udzakhala ndi zidzukulu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene kudanenedwa za iye, kuti, Mwa Isaki mbeu yako idzaitanidwa:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Za mwana ameneyu Mulungu anamuwuza iye kuti, “Zidzukulu zako zidzachokera mwa Isake.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene kudanenedwa za iye, kuti, Mwa Isake mbeu yako idzaitanidwa: