Hebrews 11:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pokhala ndi chikhulupiriro, makolo anthu akale aja Mulungu adaonetsa kuti ankakondwera nawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti momwemo akulu anachitidwa umboni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi chikhulupiriro chimenechi makolo athu akale anayamikidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti momwemo akulu anacitidwa umboru.