Hebrews 11:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pokhala ndi chikhulupiriro, Yosefe ali pafupi kutsirizika, adanenapo za kutuluka kwa Aisraele mu Ejipito, naŵauziratu za m'mene adaayenera kudzachitira ndi mafupa ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi chikhulupiriro, Yosefe, pakumwalira, anatchula za matulukidwe a ana a Israele; nalamula za mafupa ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi chikhulupiriro Yosefe ali pafupi kumwalira anayankhula za kutuluka kwa Aisraeli mu Igupto ndipo anawawuza zoti adzachite ndi mafupa ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi cikhulupiriro, Yosefe, pakumwalira, anachula za maturukidwe a ana a Israyeli; nalamulira za mafupa ace.