Hebrews 11:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazi ena adalandiranso anthu ao amene adafa, ataŵaukitsa. Ena adazunzidwa koopsa mpaka kufa, osalola kuti aŵamasule, chifukwa chofuna kudzaukanso ndi moyo wabwino kopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akazi analandira akufa ao mwa kuuka kwa akufa; ndipo ena anakwapulidwa, osalola kuomboledwa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amayi ena analandira anthu awo amene anafa, ataukitsidwanso. Enanso anazunzidwa ndipo anakana kumasulidwa, kuti adzaukenso ndi moyo wabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
16 Akazi analandira akufa ao mwa kuuka kwa akufa; ndipo 17 ena anakwapulidwa, osalola kuomboledwa,