Hebrews 11:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena, anthu adaŵaseka ndi kuŵakwapula. Adamangidwa ndi maunyolo naponyedwa m'ndende.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti akalandire kuuka koposa; koma ena anayesedwa ndi matonzo ndi zokwapulira, ndiponso nsinga, ndi kuwatsekera m'ndende;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena anawaseka ndi kuwakwapula, pamenenso ena anamangidwa ndi kupita ku ndende.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti akalandire kuuka koposa; koma ena anayesedwa ndi matonzo ndi zokwapulira, ndiponso nsinga, ndi 18 kuwatsekera m'ndende;