Hebrews 11:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ameneŵa, pansi pano sipadaŵayenere! Ankangoyenda m'zipululu ndi m'mapiri namabisala m'mapanga ndi m'maenje apansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(amenewo dziko lapansi silinayenera iwo), osokerera m'mapululu, ndi m'mapiri, ndi m'mapanga, ndi m'mauna a dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko lapansi silinawayenere. Anayendayenda mʼzipululu ndi mapiri, ndiponso mʼmapanga ndi mʼmaenje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(amenewo dziko lapansi silinayenera iwo), osokerera m'mapululu, ndi m'mapiri, ndi 20 m'mapanga, ndi m'mauna a dziko.