Hebrews 12:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti lidaaŵaopsa lamulo lija lakuti, “Ndi nyama yomwe ikangokhudza phirilo, iphedwe ndi miyala.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti sanakhoza kulola cholamulidwacho. Ingakhale nyama ikakhudza phirilo, idzaponyedwa miyala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anachita mantha ndi lamulo lija lakuti, “Ngakhale nyama ikangokhudza phirilo, iphedwe ndi miyala.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti sanakhoza kulola colamulidwaco. Ingakhale nyama ikakhudza phirilo, idzaponyedwa miyala;