Hebrews 12:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maonekedwe a zonsezo anali oopsa kwambiri, kotero kuti Mose yemwe adaati, “Ndikunjenjemera ndi mantha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo maonekedwewo anali oopsa otere, kuti Mose anati, Ndiopatu ndi kunthunthumira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maonekedwenso a Mose anali woopsa kwambiri, ngakhale Mose yemwe anati, “Ine ndinachita mantha ndi kunjenjemera.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo maonekedwewo anali oopsa otere, kuti Mose anati, Ndiopatu ndi kunthunthumira.