Hebrews 13:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tili ndi guwa, ndipo ansembe otumikira m'chihema chachipembedzo cha Ayuda saloledwa kudyako zoperekedwa pamenepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tili nalo guwa la nsembe, limene iwo akutumikira chihema alibe ulamuliro wa kudyako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tili ndi guwa lansembe, ndipo ansembe otumikira mʼtenti cha Ayuda, saloledwa kudya zochokera pamenepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tiri nalo guwa la nsembe, limene iwo akutumikira cihema alibe ulamuliro wa kudyako.