Hebrews 13:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja ife tilibe mzinda wokhazikika pansi pano, tikufunafuna wina umene ulikudza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti pano tilibe mudzi wokhalitsa, komatu tifunafuna ulinkudzawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ife tilibe mzinda wokhazikika koma tikudikira mzinda umene ukubwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti pano tiribe mudzi wokhalitsa, komatu tifunafuna ulinkudzawo.