Hebrews 13:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukupemphani makamaka kuti mupemphere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndikudandaulirani koposa kuchita ichi, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikukupemphani kuti mundipempherere kuti Mulungu andibwezere kwa inu msanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndikudandaulirani koposa kucita ici, kuti kubwera kwanga kwa inu kufulumidwe.