Hebrews 13:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musanyozere kumalandira bwino alendo m'nyumba mwanu. Pali ena amene kale adaalandira bwino alendo, ndipo mosazindikira adaalandira angelo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musaiwale kuchereza alendo; pakuti mwa ichi ena anachereza angelo osachidziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musayiwale kusamalira alendo, pakuti pochita zimenezi anthu ena anasamalira angelo amene samawadziwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musaiwale kucereza alendo; pakuti mwa ici ena anacereza angelo osacidziwa.