Hebrews 2:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ponena mau akuti, “Ndidzasimbira abale anga za dzina lanu. Ndidzakutamandani pa msonkhano wa anthu anu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi kuti, Ndidzalalikira dzina lanu kwa abale anga, pakati pa Mpingo ndidzakuimbirani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akuti, “Ine ndidzawuza abale anga za dzina lanu. Ndidzakuyimbirani nyimbo zamatamando pamaso pa mpingo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuti, ndidzalalikira dzina lanu kwa abale anga, Pakati pa Mpingo ndidzakuyimbirani.