Hebrews 2:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amanenanso kuti, “Ndidzakhulupirira Mulungu.” Penanso amanena kuti, “Ine ndili pano, pamodzi ndi ana amene Mulungu adandipatsa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso, Ndidzamtama Iye. Ndiponso, Taonani, Ine ndi ana amene Mulungu anandipatsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiponso, “Ine ndidzakhulupirira Iyeyo.” Ndiponso Iye akuti, “Ine ndili pano pamodzi ndi ana amene Mulungu wandipatsa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso, Ndidzamtama Iye. Ndiponso, Taonani, Ine ndi ana amene Mulungu anandipatsa,