Hebrews 2:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pena pake wina adanenetsa m'Malembo kuti, “Kodi munthu nchiyani, kuti muzimkumbukira, mwana wa munthu nchiyani, kuti muzimsamala?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma wina anachita umboni pena, nati, Munthu nchiyani kuti mumkumbukira iye? Kapena mwana wa munthu kuti mucheza naye?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma palipo pena pamene wina anachitira umboni kuti, “Kodi munthu ndani kuti muzimukumbukira, kapena mwana wa munthu kuti muzimusamalira?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma wina anacita umboni pena, nati, Munthu nciani kuti mumkumbukila iye? Kapena mwana wa munthu kuti muceza naye?