Hebrews 2:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo mudampatsa ulamuliro pa zinthu zonse.” Tsono ngati Mulungu adapatsa munthu ulamuliro pa zinthu zonse, palibe kanthu kamene sikali mu ulamuliro wake. Komabe m'mene zinthu ziliri tsopano sitikuwona kuti zonse zakhaladi mu ulamuliro wakewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ake. Pakuti muja adagonjetsa zonse kwa iye, sanasiyapo kanthu kosamgonjera iye. Koma sitinayamba tsopano apa kuona zonse zimgonjera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munamupatsa ulamuliro pa zinthu zonse.” Poyika zinthu zonse pansi pa ulamuliro wake, Mulungu sanasiye kanthu kamene sikali mu ulamuliro wake. Koma nthawi ino sitikuona zinthu pansi pa ulamuliro wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudagonjetsa zonse pansi pa mapaziace. Pakuti muja adagonietsa zonse kwa iye, sanasiyapo kanthu kosamgoniera iye. Koma sitinayamba tsopano apa kuona zonse zimgonjera.