Hebrews 3:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndili wokwiya ndidalumbira kuti, ‘Sadzaloŵa konse mu mpumulo umene ndidaŵakonzera.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga ndinalumbira m'ukali wanga: Ngati adzalowa mpumulo wanga!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Ine ndinalumbira nditakwiya kuti, ‘Iwo sadzalowa mu mpumulo wanga.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga ndinalumbira m'ukali wanga: Ngati adzalowa mpumulo wanga!