Hebrews 3:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga amene Mulungu adaaŵakwiyira zaka makumi anai, ndani? Ndi anthu amene adaachimwa aja, mitembo yao nkutsalira m'chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakwiya ndi ayani zaka makumi anai? Kodi si ndi awo adachimwawo, amene matupi ao adagwa m'chipululu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nanga amene Mulungu anawakwiyira zaka makumi anayi anali ndani? Kodi si anthu amene anachimwa, amene mitembo yawo inatsala mʼchipululu muja?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakwiya ndi ayani zaka makumi anai? Kodi si ndi awo adacimwawo, amene matupi ao adagwa m'cipululu?