Hebrews 3:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero tikuwona kuti anthuwo sadathe kuloŵa, chifukwa cha kusakhulupirira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Si awo kodi osamverawo? Ndipo tiona kuti sanakhoza kulowa chifukwa cha kusakhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono ife tikuona kuti sanalowe chifukwa cha kusakhulupirika kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Si awo kodiosamverawo? Ndipo tiona kuti sanakhoza kulowa cifukwa ca kusakhulupirira.