Hebrews 3:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu akuti, Pamene paja, makolo anu adaandiputa pakundiyesa, ndipo adaona zimene ndidaŵachita pa zaka makumi anai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chimene makolo anu anandiyesa nacho, ndi kundivomereza, naona ntchito zanga zaka makumi anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene makolo anu anandiputa ndi kundiyesa, ndipo kwa zaka makumi anayi anaona zimene Ine ndinachita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimene makolo anu anandiyesa naco, Ndi kundibvomereza, Naona nchito zanga zaka makumi anai.