Hebrews 4:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lonjezo la Mulungu lakuti tidzaloŵa mu mpumulo umene Iye adatikonzera, lilipobe. Tsono tichenjere kuti pasakhale wina aliyense mwa inu wopezeka kuti walephera kuloŵamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake tiope kuti kapena likatsala lonjezano lakulowa mpumulo wake, wina wa inu angaoneke ngati adaliperewera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza lonjezo lakuti tidzalowe mu mpumulo umene anatilonjeza lilipobe, tiyeni tisamale kuti pasakhale wina aliyense mwa inu wodzalephera kulowamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace tiope kuti kapena likatsala lonjezano lakulowa mpumulo wace, wina wa inu angaoneke ngati adaliperewera.