Hebrews 4:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Sadzaloŵa konse mu mpumulo umene ndidaŵakonzera.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa ndime inonso akunena za zomwezo pamene akuti, “Iwo sadzalowa konse mu mpumulo wanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'menemonso, Ngati adzalowa mpumulo wanga.