Hebrews 4:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adakonza kuti ena aloŵe ndithu mu mpumulowo, koma aja adaamva Uthenga Wabwino poyambaŵa sadaloŵemo chifukwa cha kusamvera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza tsono patsala kuti ena akalowa momwemo, ndi iwo amene Uthenga Wabwino unalalikidwa kwa iwo kale sanalowamo chifukwa cha kusamvera,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza kwatsalabe kuti ena adzalowe mu mpumulowo, koma aja anayamba kumva Uthenga Wabwino sanalowe chifukwa cha kusamvera kwawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza tsono patsala kuti ena akalowa momwemo, ndi iwo amene Uthenga Wabwino unalalikidwa kwa iwo kale sanalowamo cifukwa ca kusamvera,