Hebrews 4:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwatu Yoswa akadaŵaloŵetsa anthuwo mu mpumulo uja, sibwenzi pambuyo pake atanena za tsiku linanso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ngati Yoswa akadawapumitsa iwo, sakadalankhula m'tsogolomo za tsiku lina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati Yoswa akanalowetsa anthu mu mpumulo, Mulungu sakananena pambuyo pake za tsiku lina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ngati Yoswa akadawapumitsa iwo, sakadalankhuia m'tsogolomo za tsiku lina.