Hebrews 4:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono mpumulo wonga wa pa Sabata waŵatsalirabe anthu a Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Momwemo utsalira mpumulo wa Sabata wa kwa anthu a Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero tsono kwatsala mpumulo wa Sabata kwa anthu a Mulungu;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Momwemo utsalira mpumulo wa Sabata wa kwa anthu a Mulungu.