Hebrews 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo Mulungu adamtchula mkulu wa ansembe onse, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
wotchedwa ndi Mulungu mkulu wa ansembe monga mwa dongosolo la Melkizedeki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Mulungu anamuyika kukhala Mkulu wa ansembe, monga mwa dongosolo la unsembe wa Melikizedeki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
wochedwa ndi Mulungu mkulu wa ansembe monga mwa dongosolo la Melikizedeke.