Hebrews 5:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tili ndi zambiri zoti nkunena pa zimenezi, koma nzovuta kufotokoza kwake, popeza kuti mwasanduka ouma mitu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Za iye tili nao mau ambiri kuwanena, ndi otilaka powatanthauzira, popeza mwagontha m'makutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tili ndi zambiri zoti tinganene pa zimenezi, koma ndi zovuta kukufotokozerani chifukwa ndinu ochedwa kuphunzira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Za iye tirinao mau ambiri kuwanena, ndiotilaka powatanthauzira, popeza mwagontha m'makutu.