Hebrews 5:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza kuti iye yemweyo ali ndi zofooka zambiri, ndiye kuti angathe kuŵalezera mtima amene ali opanda nzeru ndi osokera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
akhale wokhoza kumva chifundo ndi osadziwa ndi olakwa, popeza iye yekhanso amazingwa ndi chifooko;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza kuti iye mwini ali ndi zofowoka zake, amatha kuwalezera mtima amene ali osadziwa ndi osochera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
akhale wokhoza kumva cifundo ndi osadziwa ndi olakwa, popeza iye yekhanso amazingwa ndi cifoko;