Hebrews 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Penanso Mulungu adati, “Ndiwe wansembe mpaka muyaya, unsembe wake wonga uja wa Melkizedeki.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawi zonse monga mwa dongosolo la Melkizedeki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo penanso anati, “Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya, monga mwa unsembe wa Melikizedeki.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawizonse Monga mwa dongosolo la Melikizedeke.