Hebrews 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adazindikira kukoma kwa mau a Mulungu, ndi mphamvu za nthaŵi imene inalikudzafika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nalawa mau okoma a Mulungu, ndi mphamvu ya nthawi ilinkudza,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Analawa kukoma kwa mawu a Mulungu ndi mphamvu za nthawi ikubwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nalawa mau okoma a Mulungu, ndi mphamvu ya nthawi irinkudza,