Hebrews 6:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu okondedwa anga, ngakhale tikunena zimenezi, sitikukukayikirani. Tikudziŵa kuti muli nazo zabwino, zolinga ku chipulumutso chanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma, okondedwa, takopeka mtima kuti za inu zili zoposa ndi zophatikana chipulumutso, tingakhale titero pakulankhula;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Okondedwa anga, ngakhale tikuyankhula zimenezi, ife tikudziwa kuti muli nazo zinthu zabwino zomwe zimabwera pamodzi ndi chipulumutso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma, okondedwa, takopeka mtima kuti za inu ziri zoposa ndi zophatikana cipulumutso, tingakhale titero pakulankhula;