Hebrews 7:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti iye anali akadali m'thupi la kholo lake Abrahamu pamene Melkizedeki adadzamchingamira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti pajapo anali m'chuuno cha atate wake, pamene Melkizedeki anakomana naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa pamene Melikizedeki anakumana ndi Abrahamu nʼkuti Levi ali mʼthupi la kholo lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti pajapo anali m'cuuno ca atate wace, pamene Melikizedeke anakomana naye.